Yesaya 2:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 M’tsiku limenelo, munthu wochokera kufumbi adzataya milungu yake yasiliva yopanda pake ndi milungu yake yagolide yopanda phindu, imene anthu anamupangira kuti aziigwadira. Adzaitayira kumene kumakhala aswiswiri* ndi mileme,+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:20 Yesaya 1, ptsa. 53-54
20 M’tsiku limenelo, munthu wochokera kufumbi adzataya milungu yake yasiliva yopanda pake ndi milungu yake yagolide yopanda phindu, imene anthu anamupangira kuti aziigwadira. Adzaitayira kumene kumakhala aswiswiri* ndi mileme,+