Yesaya 2:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Kuti zinthu zikuyendereni bwino, musadalire munthu wochokera kufumbi amene mpweya wake uli m’mphuno mwake,+ pakuti palibe chifukwa choti mum’ganizire iyeyo.+
22 Kuti zinthu zikuyendereni bwino, musadalire munthu wochokera kufumbi amene mpweya wake uli m’mphuno mwake,+ pakuti palibe chifukwa choti mum’ganizire iyeyo.+