Yesaya 3:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Tamverani! Ambuye woona,+ Yehova wa makamu, akuchotsa mu Yerusalemu+ ndi mu Yuda zinthu zonse zofunika pa moyo. Akuchotsa mkate, madzi,+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:1 Yesaya 1, ptsa. 56-57
3 Tamverani! Ambuye woona,+ Yehova wa makamu, akuchotsa mu Yerusalemu+ ndi mu Yuda zinthu zonse zofunika pa moyo. Akuchotsa mkate, madzi,+