-
Yesaya 3:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Iye adzakweza mawu ake m’tsiku limenelo n’kunena kuti: “Ine sindikufuna kukhala womanga zilonda ndipo m’nyumba mwanga mulibe mkate kapena nsalu. Musandiike kuti ndikhale wolamulira anthuwa.”
-