Yesaya 3:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 M’tsiku limenelo Yehova adzachotsa zokongoletsera zawo zonse: zibangili za m’miyendo, zinthu zomanga kumutu, zodzikongoletsera zooneka ngati mwezi,+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:18 Nsanja ya Olonda,7/15/2003, tsa. 28
18 M’tsiku limenelo Yehova adzachotsa zokongoletsera zawo zonse: zibangili za m’miyendo, zinthu zomanga kumutu, zodzikongoletsera zooneka ngati mwezi,+