Yesaya 4:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Yehova, pogwiritsa ntchito mzimu wa chiweruzo ndi mzimu wa moto,+ adzatsuka nyansi za ana aakazi a Ziyoni,+ ndiponso adzatsuka+ mkati mwa Yerusalemu n’kuchotsamo magazi amene Yerusalemuyo anakhetsa.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:4 Yesaya 1, ptsa. 69-70
4 Yehova, pogwiritsa ntchito mzimu wa chiweruzo ndi mzimu wa moto,+ adzatsuka nyansi za ana aakazi a Ziyoni,+ ndiponso adzatsuka+ mkati mwa Yerusalemu n’kuchotsamo magazi amene Yerusalemuyo anakhetsa.+