Yesaya 8:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Inu mitundu ya anthu, vulazani anthu, koma inuyo muphwanyidwaphwanyidwa. Inu nonse amene muli kumalekezero a dziko lapansi, tamverani.+ Nyamulani zida zankhondo+ koma muphwanyidwaphwanyidwa.+ Nyamulani zida zankhondo koma muphwanyidwaphwanyidwa. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:9 Yesaya 1, tsa. 114 Nsanja ya Olonda,4/1/1987, ptsa. 19-20
9 Inu mitundu ya anthu, vulazani anthu, koma inuyo muphwanyidwaphwanyidwa. Inu nonse amene muli kumalekezero a dziko lapansi, tamverani.+ Nyamulani zida zankhondo+ koma muphwanyidwaphwanyidwa.+ Nyamulani zida zankhondo koma muphwanyidwaphwanyidwa.