Yesaya 8:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 “Anthu inu musamanene kuti: ‘Chiwembu!’ pa nkhani zonse zimene anthu awa amanena kuti: ‘Chiwembu!’+ Musamaope zimene iwo amaopa ndipo musamanjenjemere nazo.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:12 Yesaya 1, tsa. 115 Nsanja ya Olonda,9/1/1987, ptsa. 20-23, 27-28
12 “Anthu inu musamanene kuti: ‘Chiwembu!’ pa nkhani zonse zimene anthu awa amanena kuti: ‘Chiwembu!’+ Musamaope zimene iwo amaopa ndipo musamanjenjemere nazo.+