Yesaya 10:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 kodi sizidzachitika kuti monga momwe ndidzachitire kwa Samariya ndi kwa milungu yake yopanda phindu,+ ndi mmenenso ndidzachitire kwa Yerusalemu ndi kwa mafano ake?’+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:11 Yesaya 1, ptsa. 146-147
11 kodi sizidzachitika kuti monga momwe ndidzachitire kwa Samariya ndi kwa milungu yake yopanda phindu,+ ndi mmenenso ndidzachitire kwa Yerusalemu ndi kwa mafano ake?’+