Yesaya 10:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Kuwala kwa Isiraeli+ kudzasanduka moto+ ndipo Woyera wake adzasanduka lawi la moto.+ Iye adzayaka n’kunyeketsa udzu wake* ndi zitsamba zake zaminga+ pa tsiku limodzi. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:17 Yesaya 1, ptsa. 149-150
17 Kuwala kwa Isiraeli+ kudzasanduka moto+ ndipo Woyera wake adzasanduka lawi la moto.+ Iye adzayaka n’kunyeketsa udzu wake* ndi zitsamba zake zaminga+ pa tsiku limodzi.