Yesaya 19:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Ndidzachititsa kuti Aiguputo ayambane ndi Aiguputo anzawo. Aliyense adzamenyana ndi m’bale wake ndipo aliyense adzamenyana ndi mnzake. Mzinda udzamenyana ndi mzinda unzake ndipo ufumu udzamenyana ndi ufumu unzake.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 19:2 Yesaya 1, ptsa. 200-202
2 “Ndidzachititsa kuti Aiguputo ayambane ndi Aiguputo anzawo. Aliyense adzamenyana ndi m’bale wake ndipo aliyense adzamenyana ndi mnzake. Mzinda udzamenyana ndi mzinda unzake ndipo ufumu udzamenyana ndi ufumu unzake.+