Yesaya 19:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Anthu amene amagwiritsira ntchito fulakesi*+ wopalapala pa ntchito yawo adzachita manyazi. Anthu owomba nsalu yoyera adzachitanso manyazi.
9 Anthu amene amagwiritsira ntchito fulakesi*+ wopalapala pa ntchito yawo adzachita manyazi. Anthu owomba nsalu yoyera adzachitanso manyazi.