Yesaya 19:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Anthu ake owomba nsalu+ adzavutika maganizo. Anthu onse ogwira ntchito yolipidwa adzamva chisoni mumtima.
10 Anthu ake owomba nsalu+ adzavutika maganizo. Anthu onse ogwira ntchito yolipidwa adzamva chisoni mumtima.