Yesaya 19:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Dziko la Yuda lidzakhala chinthu choopseza Iguputo.+ Aliyense amene wauzidwa za dzikolo, akuchita mantha chifukwa cha zimene Yehova wa makamu watsimikiza kuwachitira.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 19:17 Yesaya 1, ptsa. 203-204
17 Dziko la Yuda lidzakhala chinthu choopseza Iguputo.+ Aliyense amene wauzidwa za dzikolo, akuchita mantha chifukwa cha zimene Yehova wa makamu watsimikiza kuwachitira.+