Yesaya 19:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 M’tsiku limenelo, Isiraeli adzakhala gawo limodzi mwa magawo atatu, pamodzi ndi Iguputo ndi Asuri,+ kutanthauza kuti adzakhala dalitso padziko lapansi,+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 19:24 Yesaya 1, ptsa. 206-207
24 M’tsiku limenelo, Isiraeli adzakhala gawo limodzi mwa magawo atatu, pamodzi ndi Iguputo ndi Asuri,+ kutanthauza kuti adzakhala dalitso padziko lapansi,+