Yesaya 21:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mtima wanga ukuthamanga. Ndikunjenjemera ndi mantha. Chisisira cha madzulo chimene ndinali kuchikonda chakhala chondichititsa mantha.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 21:4 Yesaya 1, ptsa. 217-218
4 Mtima wanga ukuthamanga. Ndikunjenjemera ndi mantha. Chisisira cha madzulo chimene ndinali kuchikonda chakhala chondichititsa mantha.+