Yesaya 21:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pakuti Yehova wandiuza kuti: “Pita, kaike mlonda pamalo ake, kuti anene zonse zimene aone.”+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 21:6 Nsanja ya Olonda,1/1/2000, tsa. 7 Yesaya 1, ptsa. 221-223