Yesaya 23:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Chita manyazi iwe Sidoni,+ ndiponso iwe malo achitetezo a m’mbali mwa nyanja, chifukwa nyanja yanena kuti: “Sindinamvepo zowawa za pobereka, ndipo sindinaberekepo. Sindinalerepo anyamata kapena anamwali.”+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 23:4 Yesaya 1, ptsa. 246-247
4 Chita manyazi iwe Sidoni,+ ndiponso iwe malo achitetezo a m’mbali mwa nyanja, chifukwa nyanja yanena kuti: “Sindinamvepo zowawa za pobereka, ndipo sindinaberekepo. Sindinalerepo anyamata kapena anamwali.”+