Yesaya 26:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 “Pakuti iye watsitsa anthu okhala pamalo okwezeka,+ okhala m’mudzi wokwezeka.+ Mudziwo wautsitsa. Wautsitsira pansi, waugwetsa mpaka pafumbi.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 26:5 Nsanja ya Olonda,3/1/2001, ptsa. 18-191/15/1988, ptsa. 15-16 Yesaya 1, ptsa. 277-279
5 “Pakuti iye watsitsa anthu okhala pamalo okwezeka,+ okhala m’mudzi wokwezeka.+ Mudziwo wautsitsa. Wautsitsira pansi, waugwetsa mpaka pafumbi.+