Yesaya 27:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ine Yehova ndine mlonda wa mundawo.+ Ndizidzauthirira nthawi zonse.+ Ndizidzaulondera usana ndi usiku kuti wina aliyense asauwononge.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 27:3 Nsanja ya Olonda,3/1/2001, ptsa. 21-22 Yesaya 1, ptsa. 284-286
3 Ine Yehova ndine mlonda wa mundawo.+ Ndizidzauthirira nthawi zonse.+ Ndizidzaulondera usana ndi usiku kuti wina aliyense asauwononge.+