Yesaya 28:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 M’tsiku limenelo, Yehova wa makamu adzakhala ngati chisoti chokongoletsera+ ndiponso ngati nkhata yamaluwa yokongola+ kwa anthu ake otsala.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 28:5 Yesaya 1, tsa. 288 Nsanja ya Olonda,6/1/1991, ptsa. 24-25
5 M’tsiku limenelo, Yehova wa makamu adzakhala ngati chisoti chokongoletsera+ ndiponso ngati nkhata yamaluwa yokongola+ kwa anthu ake otsala.+