Yesaya 28:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Adzakhalanso ngati mzimu wa chilungamo kwa munthu wopereka chiweruzo,+ ndiponso adzakhala ngati mphamvu kwa anthu opitikitsa adani amene afika pachipata kudzamenyana nawo.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 28:6 Nsanja ya Olonda,6/1/1991, ptsa. 24-25
6 Adzakhalanso ngati mzimu wa chilungamo kwa munthu wopereka chiweruzo,+ ndiponso adzakhala ngati mphamvu kwa anthu opitikitsa adani amene afika pachipata kudzamenyana nawo.+