Yesaya 28:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Nthawi iliyonse imene akudutsa, azidzakutengani anthu inu+ chifukwa azidzadutsa m’mawa uliwonse. Azidzadutsanso usana ndi usiku ndipo adzangokhala chinthu chonjenjemeretsa,+ kuti ena amvetse uthenga umene wanenedwa.” Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 28:19 Yesaya 1, tsa. 294 Nsanja ya Olonda,6/1/1991, ptsa. 19-20
19 Nthawi iliyonse imene akudutsa, azidzakutengani anthu inu+ chifukwa azidzadutsa m’mawa uliwonse. Azidzadutsanso usana ndi usiku ndipo adzangokhala chinthu chonjenjemeretsa,+ kuti ena amvetse uthenga umene wanenedwa.”