-
Yesaya 28:20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 Pakuti bedi lafupika kwambiri moti munthu sangathe kugonapo mowongoka bwinobwino, ndipo nsalu yofunda yachepa kwambiri moti sikukwanira kuti munthu afunde bwinobwino.
-