Yesaya 28:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Kodi tirigu amene ali popunthira mbewu, amamuphwanya? Munthu samangokhalira kupuntha tiriguyo mosalekeza.+ Iye amayendetsa magudumu ake opunthira, ndi mahatchi ake, koma saphwanya tiriguyo.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 28:28 Yesaya 1, ptsa. 296, 301
28 Kodi tirigu amene ali popunthira mbewu, amamuphwanya? Munthu samangokhalira kupuntha tiriguyo mosalekeza.+ Iye amayendetsa magudumu ake opunthira, ndi mahatchi ake, koma saphwanya tiriguyo.+