Yesaya 29:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 “Tsoka kwa Ariyeli!*+ Tsoka kwa Ariyeli, tauni imene Davide anamangako msasa.+ Anthu inu, pitirizani kuchita zikondwerero+ zanu chaka ndi chaka. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 29:1 Yesaya 1, ptsa. 296-297
29 “Tsoka kwa Ariyeli!*+ Tsoka kwa Ariyeli, tauni imene Davide anamangako msasa.+ Anthu inu, pitirizani kuchita zikondwerero+ zanu chaka ndi chaka.