Yesaya 31:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Thanthwe lake lidzachoka chifukwa cha mantha ndipo akalonga ake adzachita mantha chifukwa cha chizindikiro,”+ akutero Yehova, amene kuwala kwake kuli mu Ziyoni ndiponso amene ng’anjo+ yake ili mu Yerusalemu. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 31:9 Yesaya 1, tsa. 328
9 Thanthwe lake lidzachoka chifukwa cha mantha ndipo akalonga ake adzachita mantha chifukwa cha chizindikiro,”+ akutero Yehova, amene kuwala kwake kuli mu Ziyoni ndiponso amene ng’anjo+ yake ili mu Yerusalemu.