Yesaya 38:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 ‘Ndi mawu anu, anthu amakhalabe ndi moyo inu Yehova, ndipo mofanana ndi wina aliyense, mzimu wanga umapeza moyo kudzera mu zochita zanu.+Inu mudzandibwezera thanzi langa n’kundisiya ndi moyo.+
16 ‘Ndi mawu anu, anthu amakhalabe ndi moyo inu Yehova, ndipo mofanana ndi wina aliyense, mzimu wanga umapeza moyo kudzera mu zochita zanu.+Inu mudzandibwezera thanzi langa n’kundisiya ndi moyo.+