Yesaya 50:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Koma Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, adzandithandiza.+ N’chifukwa chake sindidzamva kuti ndanyozeka. Pa chifukwa chimenechi ndalimbitsa nkhope yanga ngati mwala wa nsangalabwi, ndipo ndikudziwa kuti sindidzachita manyazi.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 50:7 Yesaya 2, tsa. 161 Nsanja ya Olonda,8/1/1995, tsa. 15
7 Koma Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, adzandithandiza.+ N’chifukwa chake sindidzamva kuti ndanyozeka. Pa chifukwa chimenechi ndalimbitsa nkhope yanga ngati mwala wa nsangalabwi, ndipo ndikudziwa kuti sindidzachita manyazi.+