Yesaya 52:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pakuti Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Poyamba anthu anga anapita ku Iguputo kuti akakhale ngati alendo.+ Ndiyeno Asuri anawapondereza popanda chifukwa.” Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 52:4 Yesaya 2, ptsa. 182-183
4 Pakuti Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Poyamba anthu anga anapita ku Iguputo kuti akakhale ngati alendo.+ Ndiyeno Asuri anawapondereza popanda chifukwa.”