Yesaya 52:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “Pa chifukwa chimenecho anthu anga adzadziwa dzina langa.+ Adzalidziwa pa chifukwa chimenecho m’tsiku limenelo, pakuti ineyo ndi amene ndikulankhula.+ Ndithu ndineyo.” Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 52:6 Yesaya 2, ptsa. 183-185
6 “Pa chifukwa chimenecho anthu anga adzadziwa dzina langa.+ Adzalidziwa pa chifukwa chimenecho m’tsiku limenelo, pakuti ineyo ndi amene ndikulankhula.+ Ndithu ndineyo.”