Yesaya 52:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 momwemonso iye adzadabwitsa mitundu yambiri.+ Mafumu adzatseka pakamwa pawo akadzamuona,+ chifukwa iwo adzaona zimene sanauzidwepo, ndipo adzaganizira zimene sanamvepo.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 52:15 Yesaya 2, tsa. 197 Galamukani!,12/8/1998, tsa. 29
15 momwemonso iye adzadabwitsa mitundu yambiri.+ Mafumu adzatseka pakamwa pawo akadzamuona,+ chifukwa iwo adzaona zimene sanauzidwepo, ndipo adzaganizira zimene sanamvepo.+