Yesaya 53:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iye adzaphuka ngati nthambi+ pamaso pa winawake, ndiponso ngati muzu m’dziko lopanda madzi. Alibe maonekedwe alionse apamwamba kapena okongola,+ ndipo maonekedwe ake si osiririka m’maso mwathu.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 53:2 Kuyankha Mafunso a M’Baibulo, Yesaya 2, ptsa. 199-200
2 Iye adzaphuka ngati nthambi+ pamaso pa winawake, ndiponso ngati muzu m’dziko lopanda madzi. Alibe maonekedwe alionse apamwamba kapena okongola,+ ndipo maonekedwe ake si osiririka m’maso mwathu.+