Yesaya 53:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Iye anapanikizidwa+ ndipo analola kuti asautsidwe,+ koma sanatsegule pakamwa pake. Anatengedwa ngati nkhosa yopita kokaphedwa,+ ndipo mofanana ndi nkhosa yaikazi imene imakhala chete akamaimeta ubweya, nayenso sanatsegule pakamwa pake.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 53:7 Kuyankha Mafunso a M’Baibulo, Nsanja ya Olonda,8/15/2011, tsa. 141/15/2009, ptsa. 27-2810/1/2008, tsa. 57/15/1996, tsa. 8
7 Iye anapanikizidwa+ ndipo analola kuti asautsidwe,+ koma sanatsegule pakamwa pake. Anatengedwa ngati nkhosa yopita kokaphedwa,+ ndipo mofanana ndi nkhosa yaikazi imene imakhala chete akamaimeta ubweya, nayenso sanatsegule pakamwa pake.+
53:7 Kuyankha Mafunso a M’Baibulo, Nsanja ya Olonda,8/15/2011, tsa. 141/15/2009, ptsa. 27-2810/1/2008, tsa. 57/15/1996, tsa. 8