Yesaya 54:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pakuti iwe udzafutukukira mbali ya kudzanja lamanja ndi kumanzere, ndipo ana ako+ adzalanda ngakhale mitundu ya anthu.+ Iwo adzakhala m’mizinda imene inasiyidwa yabwinja.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 54:3 Yesaya 2, ptsa. 221, 222-223
3 Pakuti iwe udzafutukukira mbali ya kudzanja lamanja ndi kumanzere, ndipo ana ako+ adzalanda ngakhale mitundu ya anthu.+ Iwo adzakhala m’mizinda imene inasiyidwa yabwinja.+