Yesaya 54:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Nsanja za pamakoma ako ndidzazimanga ndi miyala ya rube, ndipo zipata zako ndidzazimanga ndi miyala yofiira ngati moto.+ Zizindikiro za m’malire ako onse ndidzazimanga ndi miyala yamtengo wapatali. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 54:12 Yesaya 2, ptsa. 227-228
12 Nsanja za pamakoma ako ndidzazimanga ndi miyala ya rube, ndipo zipata zako ndidzazimanga ndi miyala yofiira ngati moto.+ Zizindikiro za m’malire ako onse ndidzazimanga ndi miyala yamtengo wapatali.