Yesaya 54:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “Inetu ndi amene ndinalenga mmisiri, amene amauzira+ moto wamakala+ n’kupanga chida chankhondo ndi luso lake. Inenso ndi amene ndinalenga munthu wowononga,+ amene amagwira ntchito yowononga ena. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 54:16 Yesaya 2, ptsa. 229-230
16 “Inetu ndi amene ndinalenga mmisiri, amene amauzira+ moto wamakala+ n’kupanga chida chankhondo ndi luso lake. Inenso ndi amene ndinalenga munthu wowononga,+ amene amagwira ntchito yowononga ena.