Yesaya 56:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Inu nyama zonse zakutchire, inu nyama zonse za m’nkhalango, bwerani mudzadye.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 56:9 Yesaya 2, tsa. 257