Yesaya 61:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Inuyo mudzatchedwa ansembe a Yehova.+ Anthu adzakutchani atumiki+ a Mulungu wathu.+ Mudzadya zinthu zochokera ku mitundu ya anthu+ ndiponso mudzalankhula za inuyo mokondwera, chifukwa cha chuma ndi ulemerero zimene mudzapeze kwa mitunduyo.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 61:6 Nsanja ya Olonda,12/15/2012, ptsa. 25-264/1/2007, tsa. 255/15/1997, tsa. 1911/1/1995, tsa. 307/1/1995, ptsa. 23-25 Yesaya 2, ptsa. 328-330
6 Inuyo mudzatchedwa ansembe a Yehova.+ Anthu adzakutchani atumiki+ a Mulungu wathu.+ Mudzadya zinthu zochokera ku mitundu ya anthu+ ndiponso mudzalankhula za inuyo mokondwera, chifukwa cha chuma ndi ulemerero zimene mudzapeze kwa mitunduyo.+
61:6 Nsanja ya Olonda,12/15/2012, ptsa. 25-264/1/2007, tsa. 255/15/1997, tsa. 1911/1/1995, tsa. 307/1/1995, ptsa. 23-25 Yesaya 2, ptsa. 328-330