Yeremiya 5:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “Kodi sindiyenera kuwalanga chifukwa cha zinthu zimenezi?” watero Yehova.+ “Kapena kodi sindiyenera kubwezera mtundu wa anthu amakhalidwe oterewa?”+ Yeremiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:9 Nsanja ya Olonda,4/1/1988, tsa. 26
9 “Kodi sindiyenera kuwalanga chifukwa cha zinthu zimenezi?” watero Yehova.+ “Kapena kodi sindiyenera kubwezera mtundu wa anthu amakhalidwe oterewa?”+