Yeremiya 5:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Aneneri nawonso akulankhula zopanda pake ndipo mwa iwo mulibe mawu a Mulungu.+ Iwo adzakhala opanda pake ngati mawu awo omwewo.”
13 Aneneri nawonso akulankhula zopanda pake ndipo mwa iwo mulibe mawu a Mulungu.+ Iwo adzakhala opanda pake ngati mawu awo omwewo.”