Yeremiya 10:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ndikonzeni, inu Yehova. Koma mundikonze ndi chiweruzo chanu+ osati mutakwiya+ chifukwa mungandifafanize.+
24 Ndikonzeni, inu Yehova. Koma mundikonze ndi chiweruzo chanu+ osati mutakwiya+ chifukwa mungandifafanize.+