-
Yeremiya 17:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Koma ine sindinaleke kukutsatirani monga m’busa wanu. Ndipo sindinalakalake kuti tsiku loopsa lifike. Inu Mulungu, mukudziwa mawu otuluka pakamwa panga chifukwa ndinawalankhula pamaso panu.
-