Yeremiya 17:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Anthu amene amandizunza achite manyazi+ koma musalole kuti ineyo ndichite manyazi.+ Anthuwo agwidwe ndi mantha aakulu koma musalole kuti ine ndigwidwe ndi mantha aakulu. Agwetsereni tsoka+ ndipo muwaphwanye kuwirikiza kawiri.+
18 Anthu amene amandizunza achite manyazi+ koma musalole kuti ineyo ndichite manyazi.+ Anthuwo agwidwe ndi mantha aakulu koma musalole kuti ine ndigwidwe ndi mantha aakulu. Agwetsereni tsoka+ ndipo muwaphwanye kuwirikiza kawiri.+