Yeremiya 19:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndiyeno Yeremiya anabwerako ku Tofeti+ kumene Yehova anamutuma kuti akalosere. Kenako anakaima m’bwalo la nyumba ya Yehova ndi kuuza anthu onse kuti:+
14 Ndiyeno Yeremiya anabwerako ku Tofeti+ kumene Yehova anamutuma kuti akalosere. Kenako anakaima m’bwalo la nyumba ya Yehova ndi kuuza anthu onse kuti:+