Yeremiya 23:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndidzapatsa nkhosazo abusa ndipo adzaziweta.+ Sizidzaopanso kanthu kapena kugwidwa ndi mantha aakulu,+ ndipo palibe imene idzasowa,” watero Yehova. Yeremiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 23:4 Yeremiya, ptsa. 129-130
4 Ndidzapatsa nkhosazo abusa ndipo adzaziweta.+ Sizidzaopanso kanthu kapena kugwidwa ndi mantha aakulu,+ ndipo palibe imene idzasowa,” watero Yehova.