Yeremiya 23:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Iwo akuganiza zochititsa anthu anga kuiwala dzina langa pogwiritsa ntchito maloto amene aneneriwo amauzana nthawi zonse,+ monga mmene makolo awo anaiwalira dzina langa chifukwa cha Baala.+ Yeremiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 23:27 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),6/2019, tsa. 4 Nsanja ya Olonda,3/1/1994, tsa. 10
27 Iwo akuganiza zochititsa anthu anga kuiwala dzina langa pogwiritsa ntchito maloto amene aneneriwo amauzana nthawi zonse,+ monga mmene makolo awo anaiwalira dzina langa chifukwa cha Baala.+