Yeremiya 23:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Koma anthu inu musanenenso kuti uthenga wa Yehova ndi katundu wolemetsa,+ pakuti mawu a aliyense wa inu ndi katundu wake wolemetsa,+ pakuti mwasintha mawu a Mulungu wathu wamoyo,+ Yehova wa makamu.
36 Koma anthu inu musanenenso kuti uthenga wa Yehova ndi katundu wolemetsa,+ pakuti mawu a aliyense wa inu ndi katundu wake wolemetsa,+ pakuti mwasintha mawu a Mulungu wathu wamoyo,+ Yehova wa makamu.