Yeremiya 23:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 tsopano ine ndikukusiyani nokhanokha anthu inu.+ Ndikusiya inuyo ndi mzinda umene ndinapatsa inu ndi makolo anu. Ndikuchita zimenezi kuti musakhalenso pamaso panga.+
39 tsopano ine ndikukusiyani nokhanokha anthu inu.+ Ndikusiya inuyo ndi mzinda umene ndinapatsa inu ndi makolo anu. Ndikuchita zimenezi kuti musakhalenso pamaso panga.+