Yeremiya 28:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 “Pita ukauze Hananiya kuti, ‘Yehova wanena kuti: “Iwe wathyola magoli+ amtengo, ndipo tsopano m’malomwake padzakhala magoli achitsulo.”+
13 “Pita ukauze Hananiya kuti, ‘Yehova wanena kuti: “Iwe wathyola magoli+ amtengo, ndipo tsopano m’malomwake padzakhala magoli achitsulo.”+